11 Solomo anatulutsa mwana wamkazi wa Farao+ mu Mzinda wa Davide+ n’kukamuika m’nyumba imene anam’mangira,+ pakuti iye anati: “Ngakhale ali mkazi wanga, asamakhale m’nyumba ya Davide mfumu ya Isiraeli, chifukwa malo alionse amene likasa la Yehova likukhala ndi oyera.”+