Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 8:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Davide anagwira amuna 1,700 okwera pamahatchi ndi amuna 20,000 oyenda pansi+ a Hadadezeri. Kenako Davide anapundula*+ mahatchi onse a magaleta+ kusiyapo mahatchi a magaleta okwana 100.

  • 2 Samueli 15:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndiyeno pambuyo pa zinthu zimenezi, Abisalomu anadzipangira galeta lokokedwa ndi mahatchi, ndipo amuna 50 anali kuthamanga patsogolo pake.+

  • 1 Mafumu 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pa nthawi imeneyi Adoniya+ mwana wa Hagiti+ anadzikweza+ n’kumati: “Ineyo ndikhala mfumu yolamulira!”+ Kenako anapangitsa galeta* lake. Analinso ndi amuna okwera pamahatchi,* ndi amuna 50 amene ankathamanga patsogolo pake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena