1 Samueli 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye anawauza kuti: “Izi ndi zimene mfumu yokulamuliraniyo izidzafuna kwa inu:+ Idzatenga ana anu+ kuti azikayenda m’magaleta*+ ake ndi kukwera pamahatchi*+ ake, ndipo ena mwa ana anuwo azidzathamanga patsogolo pa magaleta ake.+ 1 Mafumu 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawi imeneyi Adoniya+ mwana wa Hagiti+ anadzikweza+ n’kumati: “Ineyo ndikhala mfumu yolamulira!”+ Kenako anapangitsa galeta* lake. Analinso ndi amuna okwera pamahatchi,* ndi amuna 50 amene ankathamanga patsogolo pake.+ Miyambo 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kodi kudzikweza kwafika? Ndiye kuti manyazinso afika.+ Koma nzeru zimakhala ndi anthu odzichepetsa.+
11 Iye anawauza kuti: “Izi ndi zimene mfumu yokulamuliraniyo izidzafuna kwa inu:+ Idzatenga ana anu+ kuti azikayenda m’magaleta*+ ake ndi kukwera pamahatchi*+ ake, ndipo ena mwa ana anuwo azidzathamanga patsogolo pa magaleta ake.+
5 Pa nthawi imeneyi Adoniya+ mwana wa Hagiti+ anadzikweza+ n’kumati: “Ineyo ndikhala mfumu yolamulira!”+ Kenako anapangitsa galeta* lake. Analinso ndi amuna okwera pamahatchi,* ndi amuna 50 amene ankathamanga patsogolo pake.+
2 Kodi kudzikweza kwafika? Ndiye kuti manyazinso afika.+ Koma nzeru zimakhala ndi anthu odzichepetsa.+