1 Mafumu 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Palibe ana a Isiraeli amene Solomo anawasandutsa akapolo,+ chifukwa iwo anali ankhondo ake, atumiki ake, akalonga ake, asilikali othandiza pa magaleta, ndiponso atsogoleri a asilikali ake oyendetsa magaleta, ndi a amuna ake okwera pamahatchi.+ 1 Mafumu 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Solomo anali kusonkhanitsa magaleta ambiri ndi mahatchi ankhondo, ndipo anakhala ndi magaleta 1,400 ndi mahatchi ankhondo 12,000.+ Zimenezi anali kuzisunga m’mizinda yake yosungiramo magaleta ndiponso pafupi ndi mfumuyo ku Yerusalemu.+
22 Palibe ana a Isiraeli amene Solomo anawasandutsa akapolo,+ chifukwa iwo anali ankhondo ake, atumiki ake, akalonga ake, asilikali othandiza pa magaleta, ndiponso atsogoleri a asilikali ake oyendetsa magaleta, ndi a amuna ake okwera pamahatchi.+
26 Solomo anali kusonkhanitsa magaleta ambiri ndi mahatchi ankhondo, ndipo anakhala ndi magaleta 1,400 ndi mahatchi ankhondo 12,000.+ Zimenezi anali kuzisunga m’mizinda yake yosungiramo magaleta ndiponso pafupi ndi mfumuyo ku Yerusalemu.+