Ekisodo 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno Mose atakhala kumeneko nthawi yaitali, mfumu ya Iguputo inamwalira.+ Koma ana a Isiraeli anapitirizabe kuvutika ndi ukapolo ndi kulira modandaula.+ Iwo anapitirizabe kulirira thandizo kwa Mulungu woona chifukwa cha ukapolowo.+ Ekisodo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Taona, ndamva kulira kwa ana a Isiraeli, komanso ndaona kupondereza kumene Aiguputo akuwapondereza.+
23 Ndiyeno Mose atakhala kumeneko nthawi yaitali, mfumu ya Iguputo inamwalira.+ Koma ana a Isiraeli anapitirizabe kuvutika ndi ukapolo ndi kulira modandaula.+ Iwo anapitirizabe kulirira thandizo kwa Mulungu woona chifukwa cha ukapolowo.+
9 Taona, ndamva kulira kwa ana a Isiraeli, komanso ndaona kupondereza kumene Aiguputo akuwapondereza.+