1 Samueli 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mmodzi mwa atumikiwo anayankha, kuti: “Inetu ndinaona luso loimba+ la mwana wa Jese wa ku Betelehemu. Iye ndi mwamuna wolimba mtima ndiponso wamphamvu,+ mwamuna wankhondo,+ wolankhula mwanzeru+ ndi wooneka bwino,+ komanso Yehova ali naye.”+ Salimo 118:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova ali kumbali yanga, sindidzaopa.+Munthu wochokera kufumbi angandichite chiyani?+ Miyambo 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Anthu oipa amathawa popanda wowathamangitsa,+ koma olungama ali ngati mkango wamphamvu umene umakhala wolimba mtima.+
18 Mmodzi mwa atumikiwo anayankha, kuti: “Inetu ndinaona luso loimba+ la mwana wa Jese wa ku Betelehemu. Iye ndi mwamuna wolimba mtima ndiponso wamphamvu,+ mwamuna wankhondo,+ wolankhula mwanzeru+ ndi wooneka bwino,+ komanso Yehova ali naye.”+
28 Anthu oipa amathawa popanda wowathamangitsa,+ koma olungama ali ngati mkango wamphamvu umene umakhala wolimba mtima.+