Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 14:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Tsopano Sauli analimbitsa ufumu wake mu Isiraeli+ ndipo anamenya nkhondo ndi adani ake onse om’zungulira. Iye anamenyana ndi Mowabu,+ ana a Amoni,+ Edomu,+ mafumu a Zoba+ ndi Afilisiti.+ Kulikonse kumene anali kutembenukira anali kuwalanga.+

  • 2 Samueli 10:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Patapita nthawi, ana a Amoni anaona kuti akhala chinthu chonunkha+ kwa Davide. Choncho anatumiza nthumwi kuti akalembe ganyu Asiriya a ku Beti-rehobu+ ndi Asiriya a ku Zoba,+ amuna 20,000 oyenda pansi. Anapitanso kwa mfumu ya ku Maaka+ ndi kulemba ganyu amuna 1,000 ndi ku Isitobu amuna 12,000.

  • 1 Mafumu 11:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Mulungu anasankha munthu winanso woti azilimbana+ ndi Solomo. Munthuyo anali Rezoni mwana wa Eliyada, yemwe anathawa kwa mbuye wake Hadadezeri,+ mfumu ya Zoba.+

  • Salimo 60:kam
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • Kwa wotsogolera nyimbo pa Duwa la Chikumbutso. Mikitamu.* Salimo la Davide. Nyimbo yophunzitsira.+ Pa nthawi imene Davide anali pankhondo ndi Aramu-naharaimu ndi Aramu-Zoba, ndipo Yowabu anabwerera ndi kukapha Aedomu 12,000 m’chigwa cha Mchere.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena