Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 26:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Tsopano mbuyanga mfumu, mvetserani mawu a mtumiki wanu: Ngati Yehova ndiye wakutumani kuti mundiukire, iye alandire nsembe yanga yambewu.+ Koma ngati ndi ana a anthu,+ atembereredwe pamaso pa Yehova,+ chifukwa andipitikitsa ndi kundichotsa lero kuti ndisamve kuti ndili pafupi ndi cholowa cha Yehova,+ mwa kundiuza kuti, ‘Pita ukatumikire milungu ina!’+

  • 2 Samueli 24:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Mkwiyo wa Yehova unayakiranso+ Isiraeli pamene winawake anaukira Isiraeli mwa kulimbikitsa Davide kuti: “Pita ukawerenge+ anthu a Isiraeli ndi Yuda.”

  • 1 Mafumu 11:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kenako Yehova anasankha munthu woti azilimbana+ ndi Solomo.+ Munthuyo dzina lake linali Hadadi, Mwedomu, mbadwa ya mfumu, ndipo anali kukhala ku Edomu.+

  • 1 Mbiri 5:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Choncho, Mulungu wa Isiraeli analimbikitsa mtima+ wa Puli+ mfumu ya Asuri,+ ndithu analimbikitsa mtima wa Tigilati-pilenesere+ mfumu ya Asuri, moti anatenga+ Arubeni, Agadi, ndi hafu ya fuko la Manase n’kuwapititsa ku Hala,+ ku Habori, ku Hara, ndi kumtsinje wa Gozani, ndipo akukhalabe kumeneko mpaka lero.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena