Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 3:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Manja ako sanali omangidwa,+

      Ndipo mapazi ako sanaikidwe m’matangadza amkuwa.+

      Wagwa ngati munthu wogwa pamaso pa anthu osalungama.”+

      Pamenepo anthu onse anamuliranso.+

  • 2 Samueli 11:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Zitatero, Davide anatuma nthumwi kukafufuza za mkaziyo.+ Ndiyeno munthu wina ananena kuti: “Kodi ameneyu si Bati-seba+ mwana wa Eliyamu,*+ mkazi wa Uriya+ Mhiti?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena