Salimo 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amadikirira anthu pamalo obisika ngati mkango pamalo ake obisalapo.+Amawadikirira+ kuti atenge mokakamiza munthu wosautsika.Amakulunga wosautsika mu ukonde wake ndi kumutenga mokakamiza.+ Salimo 55:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mawu a pakamwa pake ndi osalala ngati mafuta a mkaka,+Koma mtima wake umakonda ndewu.+Mawu ake ndi osalala ngati mafuta,+Koma ali ngati lupanga lakuthwa.+ Miyambo 26:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ngakhale azilankhula mawu okoma,+ usam’khulupirire+ chifukwa mumtima mwake muli zinthu 7 zonyansa.+
9 Amadikirira anthu pamalo obisika ngati mkango pamalo ake obisalapo.+Amawadikirira+ kuti atenge mokakamiza munthu wosautsika.Amakulunga wosautsika mu ukonde wake ndi kumutenga mokakamiza.+
21 Mawu a pakamwa pake ndi osalala ngati mafuta a mkaka,+Koma mtima wake umakonda ndewu.+Mawu ake ndi osalala ngati mafuta,+Koma ali ngati lupanga lakuthwa.+
25 Ngakhale azilankhula mawu okoma,+ usam’khulupirire+ chifukwa mumtima mwake muli zinthu 7 zonyansa.+