2 Samueli 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndimupeza ali wotopa ndi wofooka manja ake onse,+ ndipo adzanjenjemera ndithu chifukwa cha ine. Pamenepo anthu onse amene ali naye adzathawa, ndipo ine ndidzapha mfumu ili yokha.+ 1 Mafumu 22:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Mfumu ya Siriya inali italamula akuluakulu ake 32+ oyang’anira asilikali okwera magaleta, kuti: “Musakamenyane ndi wina aliyense, wamng’ono kapena wamkulu, koma mfumu ya Isiraeli yokha basi.”+
2 Ndimupeza ali wotopa ndi wofooka manja ake onse,+ ndipo adzanjenjemera ndithu chifukwa cha ine. Pamenepo anthu onse amene ali naye adzathawa, ndipo ine ndidzapha mfumu ili yokha.+
31 Mfumu ya Siriya inali italamula akuluakulu ake 32+ oyang’anira asilikali okwera magaleta, kuti: “Musakamenyane ndi wina aliyense, wamng’ono kapena wamkulu, koma mfumu ya Isiraeli yokha basi.”+