Yoswa 18:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mizipe,+ Kefira,+ Moza, Oweruza 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chotero ana onse a Isiraeli anatuluka,+ kuchokera ku Dani+ mpaka kumunsi ku Beere-seba,+ ndipo khamu lonselo linasonkhana pamodzi mogwirizana+ kwa Yehova ku Mizipa,+ pamodzinso ndi anthu a m’dera la Giliyadi.+ 1 Samueli 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Samueli anawauza kuti: “Sonkhanitsani Aisiraeli onse+ pamodzi ku Mizipa,+ kuti ndikupempherereni+ kwa Yehova.” Yeremiya 40:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero Yeremiya anapita ku Mizipa+ kukakhala ndi Gedaliya+ mwana wa Ahikamu pakati pa anthu amene anatsala m’dzikolo.
20 Chotero ana onse a Isiraeli anatuluka,+ kuchokera ku Dani+ mpaka kumunsi ku Beere-seba,+ ndipo khamu lonselo linasonkhana pamodzi mogwirizana+ kwa Yehova ku Mizipa,+ pamodzinso ndi anthu a m’dera la Giliyadi.+
5 Ndiyeno Samueli anawauza kuti: “Sonkhanitsani Aisiraeli onse+ pamodzi ku Mizipa,+ kuti ndikupempherereni+ kwa Yehova.”
6 Chotero Yeremiya anapita ku Mizipa+ kukakhala ndi Gedaliya+ mwana wa Ahikamu pakati pa anthu amene anatsala m’dzikolo.