Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 3:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pamenepo Yehosafati anati:+ “Kodi kuno kulibe mneneri wa Yehova?+ Ngati alipo tiyeni tifunsire kwa Yehova kudzera mwa iye.”+ Ndiyeno mmodzi mwa atumiki a mfumu ya Isiraeli anayankha kuti: “Kuli Elisa+ mwana wa Safati, amene anali kuthirira Eliya madzi osamba m’manja.”+

  • 2 Mbiri 18:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Koma Yehosafati anati: “Kodi kuno kulibe mneneri wina wa Yehova amene watsala?+ Ngati alipo, tiyeni tifunse kudzera mwa ameneyo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena