Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Mukatero mutenge kamtengo ka hisope+ n’kukaviika m’beseni la magazi ndi kuwaza pafelemu la pamwamba pa chitseko, ndipo ena mwa magaziwo muwaze pamafelemu awiri a m’mbali mwa khomo. Aliyense asatuluke m’nyumba yake mpaka m’mawa.

  • Numeri 19:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ndiyeno munthu wosadetsedwa+ atenge kamtengo ka hisope.+ Akaviike m’madziwo n’kuwaza hemalo. Awazenso ziwiya zonse ndi anthu onse amene anali muhemalo. Komanso, awaze munthu amene anakhudza fupa la munthu, kapena kukhudza munthu wophedwa, kapenanso mtembo uliwonse, ngakhalenso manda a munthu.

  • Salimo 51:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Ndiyeretseni ndi hisope ku machimo anga kuti ndikhale woyera.+

      Ndisambitseni kuti ndiyere kwambiri kuposa chipale chofewa.+

  • Aheberi 9:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Pakuti pamene Mose anatchulira anthu onsewo lamulo lililonse malinga ndi Chilamulo,+ anatenga magazi a ng’ombe zazing’ono zamphongo ndi magazi a mbuzi, pamodzi ndi madzi, ubweya wa nkhosa wofiira kwambiri, ndi timitengo ta hisope,+ n’kuwaza bukulo ndi anthu onse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena