26 Iye anatenga chuma cha m’nyumba ya Yehova ndi chuma cha m’nyumba ya mfumu.+ Anatenga chilichonse+ kuphatikizapo zishango zonse zagolide zimene Solomo anapanga.+
9 Chotero Sisaki+ mfumu ya Iguputo anaukira Yerusalemu ndi kutenga chuma cha m’nyumba ya Yehova+ ndi chuma cha m’nyumba ya mfumu.+ Anatenga chilichonse kuphatikizapo zishango zagolide zimene Solomo anapanga.+