Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 49:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Yuda ndi mwana wa mkango.+ Umapha nyama n’kubwerako ndithu, mwana wanga. Iye amapinda mawondo ake n’kudziwongola ngati mkango utagona pansi. Ndipo monga mkango, ndani angamudzutse?+

  • Numeri 23:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Taonani, mtundu udzadzuka ngati mkango,

      Udzanyamuka monga mkango.+

      Sugona pansi mpaka ugwire nyama,

      Ndipo udzamwa magazi a ophedwawo.”+

  • Numeri 24:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Iye anagwada pansi. Anagona pansi ngati mkango.

      Ngati mkango, ndani angayese kum’dzutsa?+

      Odalitsa iwe n’ngodalitsika,+

      Ndipo otemberera iwe n’ngotembereredwa.”+

  • Miyambo 28:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Anthu oipa amathawa popanda wowathamangitsa,+ koma olungama ali ngati mkango wamphamvu umene umakhala wolimba mtima.+

  • Chivumbulutso 5:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Koma mmodzi wa akulu aja anandiuza kuti: “Tonthola. Taona! Mkango wa fuko la Yuda,+ muzu+ wa Davide,+ anapambana pa nkhondo+ moti iye ndiye woyenera kumatula zidindo 7 zimene amatira mpukutuwo ndi kuutsegula.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena