2 Mbiri 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova anapitiriza kukhala ndi Yehosafati+ chifukwa anayenda m’njira zimene Davide kholo lake+ anayenda kalekale, ndipo sanafunefune Abaala.+ 2 Mbiri 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehosafati anapitiriza kukhala ku Yerusalemu. Iye anayambanso kupita pakati pa anthu, kuyambira ku Beere-seba+ mpaka kudera lamapiri la Efuraimu,+ kuti awabwezere kwa Yehova Mulungu wa makolo awo.+
3 Yehova anapitiriza kukhala ndi Yehosafati+ chifukwa anayenda m’njira zimene Davide kholo lake+ anayenda kalekale, ndipo sanafunefune Abaala.+
4 Yehosafati anapitiriza kukhala ku Yerusalemu. Iye anayambanso kupita pakati pa anthu, kuyambira ku Beere-seba+ mpaka kudera lamapiri la Efuraimu,+ kuti awabwezere kwa Yehova Mulungu wa makolo awo.+