Miyambo 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Amene amalangiza wonyoza amadzichotsera yekha ulemu,+ ndipo amene amadzudzula woipa amadzibweretsera chilema.+ Miyambo 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Usayankhe aliyense wopusa mogwirizana ndi uchitsiru wake, kuti iweyo usafanane naye.+ Yesaya 36:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anthuwo anangokhala chete osamuyankha,+ chifukwa lamulo lochokera kwa mfumu linali lakuti: “Musamuyankhe.”+ 2 Timoteyo 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kapolo wa Ambuye sayenera kukangana ndi anthu,+ koma ayenera kukhala wodekha kwa onse.+ Ayeneranso kukhala woyenerera kuphunzitsa,+ wougwira mtima pokumana ndi zoipa,+
7 Amene amalangiza wonyoza amadzichotsera yekha ulemu,+ ndipo amene amadzudzula woipa amadzibweretsera chilema.+
21 Anthuwo anangokhala chete osamuyankha,+ chifukwa lamulo lochokera kwa mfumu linali lakuti: “Musamuyankhe.”+
24 Kapolo wa Ambuye sayenera kukangana ndi anthu,+ koma ayenera kukhala wodekha kwa onse.+ Ayeneranso kukhala woyenerera kuphunzitsa,+ wougwira mtima pokumana ndi zoipa,+