Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 38:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma ine ndakhala ngati munthu wogontha, sindikumvetsera,+

      Ndakhala ngati munthu wosalankhula, sindikutsegula pakamwa.+

  • Salimo 38:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndakhala ngati munthu wosamva,

      Sindikulankhula zotsutsana nawo.

  • Salimo 39:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Ine ndinati: “Ndidzatchinjiriza njira zanga,+

      Kuti ndisachimwe ndi lilime langa.+

      Ndidzamanga pakamwa panga kuti patetezeke,+

      Nthawi zonse pamene woipa ali pamaso panga.”+

  • Miyambo 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Amene amalangiza wonyoza amadzichotsera yekha ulemu,+ ndipo amene amadzudzula woipa amadzibweretsera chilema.+

  • Miyambo 26:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Usayankhe aliyense wopusa mogwirizana ndi uchitsiru wake, kuti iweyo usafanane naye.+

  • Mateyu 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Musamapatse agalu zinthu zopatulika,+ kapena kuponyera nkhumba ngale zanu, kuopera kuti zingapondeponde ngalezo+ kenako n’kutembenuka ndi kukukhadzulani.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena