Yeremiya 32:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Kalanga ine! Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.+ Inuyo ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi pogwiritsa ntchito mphamvu yanu+ ndi dzanja lanu lotambasula.+ Nkhaniyi si yovuta kwa inu.+ Maliko 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yesu anawayang’ana ndi kuwauza kuti: “Kwa anthu n’zosathekadi, koma sizili choncho kwa Mulungu, pakuti zinthu zonse n’zotheka ndi Mulungu.”+
17 “Kalanga ine! Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.+ Inuyo ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi pogwiritsa ntchito mphamvu yanu+ ndi dzanja lanu lotambasula.+ Nkhaniyi si yovuta kwa inu.+
27 Yesu anawayang’ana ndi kuwauza kuti: “Kwa anthu n’zosathekadi, koma sizili choncho kwa Mulungu, pakuti zinthu zonse n’zotheka ndi Mulungu.”+