-
Yeremiya 51:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 “Kwezani mtengo wa chizindikiro amuna inu.+ Imbani lipenga pakati pa mitundu ya anthu. Konzekeretsani+ mitundu ya anthu yoti imuthire nkhondo. Muitanireni maufumu a ku Ararati,+ ku Mini ndi ku Asikenazi.+ Muikireni wolemba anthu usilikali. Mubweretsereni mahatchi+ ngati dzombe lokhala ndi ubweya.
-