Yoswa 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa tsiku limene Yehova anapereka Aamori kwa ana a Isiraeli, Yoswa analankhula ndi Yehova pamaso pa Aisiraeli kuti:“Dzuwa iwe,+ ima pamwamba pa Gibeoni,+Ndipo iwe mwezi, ima pamwamba pa chigwa cha Aijaloni.”+ 2 Mbiri 32:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiyeno zinachitika kuti pamene akalonga a ku Babulo+ anatumiza nthumwi zawo kwa iye,+ kuti zikam’funse za chizindikiro cholosera zam’tsogolo+ chimene chinachitika m’dzikolo, Mulungu woona anamusiya+ kuti amuyese+ ndi kuona zonse zimene zinali mumtima mwake.+ Yesaya 38:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndichititsa mthunzi wa dzuwa+ umene wapita kale kutsogolo pamasitepe a Ahazi, kuti ubwerere m’mbuyo masitepe 10.”’”+ Choncho dzuwa linabwerera m’mbuyo pang’onopang’ono masitepe 10 pa masitepe pomwe linali litapita kale kutsogolo.+
12 Pa tsiku limene Yehova anapereka Aamori kwa ana a Isiraeli, Yoswa analankhula ndi Yehova pamaso pa Aisiraeli kuti:“Dzuwa iwe,+ ima pamwamba pa Gibeoni,+Ndipo iwe mwezi, ima pamwamba pa chigwa cha Aijaloni.”+
31 Ndiyeno zinachitika kuti pamene akalonga a ku Babulo+ anatumiza nthumwi zawo kwa iye,+ kuti zikam’funse za chizindikiro cholosera zam’tsogolo+ chimene chinachitika m’dzikolo, Mulungu woona anamusiya+ kuti amuyese+ ndi kuona zonse zimene zinali mumtima mwake.+
8 Ndichititsa mthunzi wa dzuwa+ umene wapita kale kutsogolo pamasitepe a Ahazi, kuti ubwerere m’mbuyo masitepe 10.”’”+ Choncho dzuwa linabwerera m’mbuyo pang’onopang’ono masitepe 10 pa masitepe pomwe linali litapita kale kutsogolo.+