2 Mbiri 29:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti makolo athu achita zosakhulupirika+ ndipo achita zoipa pamaso pa Yehova Mulungu wathu.+ Iwo anamusiya+ n’kufulatira chihema chopatulika cha Yehova+ n’kulozetsako nkhongo. Salimo 106:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tachimwa mofanana ndi makolo athu.+Tachita zinthu zosayenera, tachita zinthu zoipa.+ Yeremiya 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndipo inu mwachita zinthu zoipa kwambiri kuposa makolo anu.+ Aliyense wa inu akupitiriza kuumitsa mtima+ wake woipawo ndipo simukundimvera.+ Danieli 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Inu Yehova, manyazi aphimba nkhope zathu, za mafumu athu, akalonga athu ndi makolo athu chifukwa takuchimwirani.+
6 Pakuti makolo athu achita zosakhulupirika+ ndipo achita zoipa pamaso pa Yehova Mulungu wathu.+ Iwo anamusiya+ n’kufulatira chihema chopatulika cha Yehova+ n’kulozetsako nkhongo.
12 Ndipo inu mwachita zinthu zoipa kwambiri kuposa makolo anu.+ Aliyense wa inu akupitiriza kuumitsa mtima+ wake woipawo ndipo simukundimvera.+
8 “Inu Yehova, manyazi aphimba nkhope zathu, za mafumu athu, akalonga athu ndi makolo athu chifukwa takuchimwirani.+