2 Mafumu 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Pita kwa Hilikiya+ mkulu wa ansembe,+ ukamuuze kuti asonkhanitse pamodzi ndalama zonse+ zimene zikubwera kunyumba ya Yehova,+ zimene alonda a pakhomo+ atolera kwa anthu. 1 Mbiri 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Salumu anabereka Hilikiya,+ Hilikiya anabereka Azariya,
4 “Pita kwa Hilikiya+ mkulu wa ansembe,+ ukamuuze kuti asonkhanitse pamodzi ndalama zonse+ zimene zikubwera kunyumba ya Yehova,+ zimene alonda a pakhomo+ atolera kwa anthu.