Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 22:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Njira ya Mulungu woona ndi yangwiro.+

      Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino.+

      Iye ndi chishango kwa onse othawira kwa iye.+

  • 2 Mbiri 32:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Limbani mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu.+ Musaope+ kapena kuchita mantha+ ndi mfumu ya Asuri+ ndi khamu lalikulu limene ili nalo,+ chifukwa ife tili ndi ambiri kuposa amene ali ndi mfumuyo.

  • Salimo 27:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Ngakhale gulu lankhondo litamanga msasa kuti lindiukire,+

      Mtima wanga sudzachita mantha.+

      Ngakhale nkhondo yolimbana ndi ine itayambika,+

      Pameneponso ndidzadalira Mulungu.+

  • Salimo 46:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Yehova wa makamu ali ndi ife.+

      Mulungu wa Yakobo ndiye malo athu okwezeka ndiponso achitetezo.+ [Seʹlah.]

  • Salimo 55:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Iye adzandiwombola ndi kundikhazika pa mtendere, kundichotsa pankhondo,+

      Pakuti khamu la anthu landiukira.+

  • Aroma 8:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena