-
2 Mafumu 7:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Tsopano Elisa anati: “Amuna inu, mverani mawu a Yehova.+ Yehova wanena kuti, ‘Mawa chapanthawi ngati ino, pachipata cha Samariya, ufa wosalala wokwana muyezo umodzi wa seya,* mtengo wake udzakhala sekeli* limodzi, ndipo balere wokwana miyezo iwiri ya seya, mtengo wake udzakhalanso sekeli limodzi.’”+
-
-
Yesaya 44:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Ndine amene ndimachititsa mawu a mtumiki wanga kukwaniritsidwa ndiponso amene ndimakwaniritsa mawu onse amene atumiki anga analengeza.+ Ndine amene ndikunena za Yerusalemu kuti, ‘Muzidzakhala anthu.’+ Ndikunenanso za mizinda ya ku Yuda kuti, ‘Idzamangidwanso,+ ndipo malo ake osakazidwa ndidzawamanganso.’+
-