-
2 Mafumu 7:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Chotero zinachitikadi monga mmene munthu wa Mulungu woona uja ananenera kwa mfumu, kuti: “Balere wokwana miyezo iwiri ya seya mtengo wake udzafika pa sekeli imodzi, ndipo ufa wosalala wokwana muyezo umodzi wa seya, mtengo wake udzafikanso pa sekeli imodzi mawa, pa nthawi ngati ino pachipata cha Samariya.”+
-