1 Samueli 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Funsa anyamata ako zimenezi ndipo akuuza. Motero uwakomere mtima anyamata anga chifukwa tabwera tsiku labwino. Chonde, ugawire atumiki ako ndi mwana wako Davide chilichonse chimene dzanja lako lingapeze.’”+ 2 Mafumu 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mfumu ya Isiraeli itangoona anthuwo, inafunsa Elisa kuti: “Kodi ndiwaphe?+ Ndiwaphe kodi bambo?”+ 2 Mafumu 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Elisa+ anadwala matenda amene pamapeto pake anafa nawo.+ Choncho Yehoasi mfumu ya Isiraeli anapita kwa iye n’kuyamba kulira atam’kumbatira n’kumati: “Bambo anga,+ bambo anga! Galeta lankhondo la Isiraeli ndi okwera pamahatchi ake!”+
8 Funsa anyamata ako zimenezi ndipo akuuza. Motero uwakomere mtima anyamata anga chifukwa tabwera tsiku labwino. Chonde, ugawire atumiki ako ndi mwana wako Davide chilichonse chimene dzanja lako lingapeze.’”+
14 Tsopano Elisa+ anadwala matenda amene pamapeto pake anafa nawo.+ Choncho Yehoasi mfumu ya Isiraeli anapita kwa iye n’kuyamba kulira atam’kumbatira n’kumati: “Bambo anga,+ bambo anga! Galeta lankhondo la Isiraeli ndi okwera pamahatchi ake!”+