1 Samueli 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno Afilisiti+ anasonkhanitsa asilikali awo onse ku Afeki, pamene Aisiraeli anamanga msasa pafupi ndi kasupe amene anali ku Yezereeli.+ 1 Mafumu 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kumayambiriro kwa chaka, Beni-hadadi anasonkhanitsa Asiriya+ n’kupita ku Afeki+ kuti akamenyane ndi Aisiraeli.
29 Ndiyeno Afilisiti+ anasonkhanitsa asilikali awo onse ku Afeki, pamene Aisiraeli anamanga msasa pafupi ndi kasupe amene anali ku Yezereeli.+
26 Kumayambiriro kwa chaka, Beni-hadadi anasonkhanitsa Asiriya+ n’kupita ku Afeki+ kuti akamenyane ndi Aisiraeli.