Deuteronomo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti ndi mtundu winanso uti wamphamvu+ umene milungu yake ili pafupi nawo, monga mmene Yehova Mulungu wathu alili pafupi ndi ife, tikamaitanira pa iye+ nthawi zonse? Deuteronomo 33:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Isiraeli adzakhala motetezeka,+Kasupe wa Yakobo adzakhala mosatekeseka,+M’dziko lokhala ndi chakudya ndi vinyo watsopano.+Ndipo kumwamba kwake kudzagwetsa mame.+ Salimo 147:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Sanachite zimenezi ndi mtundu wina uliwonse,+Ndipo mitundu inayo sikudziwa zigamulo zake.+Tamandani Ya, anthu inu!+
7 Pakuti ndi mtundu winanso uti wamphamvu+ umene milungu yake ili pafupi nawo, monga mmene Yehova Mulungu wathu alili pafupi ndi ife, tikamaitanira pa iye+ nthawi zonse?
28 Isiraeli adzakhala motetezeka,+Kasupe wa Yakobo adzakhala mosatekeseka,+M’dziko lokhala ndi chakudya ndi vinyo watsopano.+Ndipo kumwamba kwake kudzagwetsa mame.+
20 Sanachite zimenezi ndi mtundu wina uliwonse,+Ndipo mitundu inayo sikudziwa zigamulo zake.+Tamandani Ya, anthu inu!+