Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Hafu ya fuko la Manase ndinalipatsa dera lotsala la Giliyadi+ ndi Basana+ yense wa ufumu wa Ogi. Kodi si paja dera lonse la Arigobi+ limene ndi Basana yense, limatchedwa dziko la Arefai?+

  • Deuteronomo 32:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Anamudyetsanso mafuta a mkaka wa ng’ombe ndi mkaka wa nkhosa,+

      Pamodzi ndi mafuta a nkhosa.

      Anamudyetsa nkhosa zamphongo za ku Basana, mbuzi zamphongo,+

      Pamodzi ndi tirigu wabwino koposa ngati mafuta okuta impso.+

      Ndipo anali kumwa magazi a mphesa monga vinyo.+

  • Yeremiya 50:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Isiraeli ndidzamubwezeretsa kumalo ake odyerako msipu+ moti adzadya msipu paphiri la Karimeli+ ndi ku Basana.+ Iye adzakhutira m’madera amapiri a Efuraimu+ ndi Giliyadi.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena