Ekisodo 30:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Aroni azipaka ena mwa magazi a nyama ya nsembe yamachimo yophimbira machimo,+ panyanga za guwalo kuti aziphimbira machimo. Azichita zimenezi kamodzi pa chaka+ m’mibadwo yanu yonse. Kwa Yehova, guwalo ndi lopatulika koposa.” 2 Mbiri 29:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano ansembe anazipha n’kuzipereka nsembe yamachimo pamodzi ndi magazi ake paguwa lansembe kuti aphimbe machimo a Aisiraeli onse,+ popeza mfumu inati nsembe yopsereza ndi yamachimoyo+ ikhale ya Aisiraeli onse.+
10 Aroni azipaka ena mwa magazi a nyama ya nsembe yamachimo yophimbira machimo,+ panyanga za guwalo kuti aziphimbira machimo. Azichita zimenezi kamodzi pa chaka+ m’mibadwo yanu yonse. Kwa Yehova, guwalo ndi lopatulika koposa.”
24 Tsopano ansembe anazipha n’kuzipereka nsembe yamachimo pamodzi ndi magazi ake paguwa lansembe kuti aphimbe machimo a Aisiraeli onse,+ popeza mfumu inati nsembe yopsereza ndi yamachimoyo+ ikhale ya Aisiraeli onse.+