Yoswa 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Aefuraimu analephera kupitikitsa Akanani+ amene anali kukhala ku Gezeri.+ Choncho Akananiwo akukhalabe pakati pa Aefuraimu mpaka lero,+ ndipo anayamba kuwagwiritsa ntchito yaukapolo.+ Yoswa 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Motero anawapatsa mzinda wothawirako+ munthu amene wapha mnzake,+ wa Sekemu,+ ndi malo ake odyetserako ziweto+ m’dera lamapiri la Efuraimu. Anawapatsanso Gezeri+ ndi malo ake odyetserako ziweto,
10 Aefuraimu analephera kupitikitsa Akanani+ amene anali kukhala ku Gezeri.+ Choncho Akananiwo akukhalabe pakati pa Aefuraimu mpaka lero,+ ndipo anayamba kuwagwiritsa ntchito yaukapolo.+
21 Motero anawapatsa mzinda wothawirako+ munthu amene wapha mnzake,+ wa Sekemu,+ ndi malo ake odyetserako ziweto+ m’dera lamapiri la Efuraimu. Anawapatsanso Gezeri+ ndi malo ake odyetserako ziweto,