Oweruza 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno anamva ludzu koopsa, ndipo anayamba kufuulira Yehova kuti: “Ndinu amene mwapereka chipulumutso chachikulu chimenechi m’manja mwa mtumiki wanu.+ Tsopano kodi ndife ndi ludzu, ndigwere m’manja mwa anthu osadulidwa?”+ 2 Samueli 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Anthu inu musanene zimenezi mumzinda wa Gati.+Musalengeze zimenezi m’misewu ya Asikeloni,+Kuopera kuti ana aakazi a Afilisiti angasangalale,+Kuopera kuti ana aakazi a anthu osadulidwa angakondwere.
18 Ndiyeno anamva ludzu koopsa, ndipo anayamba kufuulira Yehova kuti: “Ndinu amene mwapereka chipulumutso chachikulu chimenechi m’manja mwa mtumiki wanu.+ Tsopano kodi ndife ndi ludzu, ndigwere m’manja mwa anthu osadulidwa?”+
20 Anthu inu musanene zimenezi mumzinda wa Gati.+Musalengeze zimenezi m’misewu ya Asikeloni,+Kuopera kuti ana aakazi a Afilisiti angasangalale,+Kuopera kuti ana aakazi a anthu osadulidwa angakondwere.