1 Samueli 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Samueli anachita zimene Yehova anamuuza. Atafika ku Betelehemu,+ akulu a mzindawo anayamba kunjenjemera+ atakumana naye. Ndiyeno iwo anati: “Kodi n’kwabwino?”+ 1 Mafumu 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Patapita nthawi, Adoniya mwana wa Hagiti anapita kwa Bati-seba,+ amayi a Solomo. Iwo atamuona, anam’funsa kuti: “Kodi mwabwerera mtendere?”+ Iye anayankha kuti: “Inde, ndabwerera mtendere.”
4 Samueli anachita zimene Yehova anamuuza. Atafika ku Betelehemu,+ akulu a mzindawo anayamba kunjenjemera+ atakumana naye. Ndiyeno iwo anati: “Kodi n’kwabwino?”+
13 Patapita nthawi, Adoniya mwana wa Hagiti anapita kwa Bati-seba,+ amayi a Solomo. Iwo atamuona, anam’funsa kuti: “Kodi mwabwerera mtendere?”+ Iye anayankha kuti: “Inde, ndabwerera mtendere.”