1 Mafumu 1:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Kuwonjezera apo, atumiki a mfumu abwera kudzafunira mafuno abwino mbuye wathu Mfumu Davide kuti: ‘Mulungu wanu akulitse dzina la Solomo kuposa dzina lanu ndiponso akweze ufumu wake kuposa ufumu wanu!’+ Kenako mfumuyo inaweramira pabedi.+ Mateyu 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Jese anabereka mfumu+ Davide.+ Davide anabereka Solomo,+ yemwe mayi ake anali mkazi wa Uriya.
47 Kuwonjezera apo, atumiki a mfumu abwera kudzafunira mafuno abwino mbuye wathu Mfumu Davide kuti: ‘Mulungu wanu akulitse dzina la Solomo kuposa dzina lanu ndiponso akweze ufumu wake kuposa ufumu wanu!’+ Kenako mfumuyo inaweramira pabedi.+