Ekisodo 29:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 “Zimene uzipereka paguwa lansembelo ndi izi: ana a nkhosa a chaka chimodzi, awiri pa tsiku nthawi zonse.+ Numeri 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lamula ana a Isiraeli kuti, ‘Muzionetsetsa kuti pa nthawi yake yoikidwiratu+ mukupereka kwa ine nsembe yanga, yomwe ndi chakudya changa+ chotentha ndi moto, chotulutsa fungo londikhazika mtima pansi.’+
38 “Zimene uzipereka paguwa lansembelo ndi izi: ana a nkhosa a chaka chimodzi, awiri pa tsiku nthawi zonse.+
2 “Lamula ana a Isiraeli kuti, ‘Muzionetsetsa kuti pa nthawi yake yoikidwiratu+ mukupereka kwa ine nsembe yanga, yomwe ndi chakudya changa+ chotentha ndi moto, chotulutsa fungo londikhazika mtima pansi.’+