Genesis 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense wokhetsa magazi a munthu, nayenso magazi ake adzakhetsedwa ndi munthu,+ chifukwa Mulungu anapanga munthu m’chifaniziro chake. Ekisodo 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Munthu amene wapsera mtima mnzake mpaka kumupha mwachiwembu,+ ngakhale atathawira kuguwa langa lansembe kuti atetezeke, muzimuchotsa n’kukamupha.+ Numeri 35:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndipo musalandire dipo lowombolera moyo wa munthu wakupha mnzake, chifukwa ndi woyenera kuphedwa.+ Aphedwe ndithu ameneyo.+
6 Aliyense wokhetsa magazi a munthu, nayenso magazi ake adzakhetsedwa ndi munthu,+ chifukwa Mulungu anapanga munthu m’chifaniziro chake.
14 Munthu amene wapsera mtima mnzake mpaka kumupha mwachiwembu,+ ngakhale atathawira kuguwa langa lansembe kuti atetezeke, muzimuchotsa n’kukamupha.+
31 Ndipo musalandire dipo lowombolera moyo wa munthu wakupha mnzake, chifukwa ndi woyenera kuphedwa.+ Aphedwe ndithu ameneyo.+