Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 16:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ana a Yosefe,+ omwe ndi Manase ndi Efuraimu,+ analandira gawo lawo.+

  • 2 Mbiri 17:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Iye anaika magulu ankhondo m’mizinda yonse ya Yuda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri. Anamanganso midzi ya asilikali m’dziko la Yuda ndi m’mizinda ya Efuraimu imene Asa bambo ake analanda.+

  • 2 Mbiri 34:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Komanso, m’mizinda ya Manase,+ Efuraimu,+ Simiyoni, mpaka Nafitali, ndi m’malo onse owonongedwa ozungulira mizindayi,

  • Hoseya 11:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Kodi ndikusiyirenji iwe Efuraimu?+ Kodi ndikuperekerenji kwa adani iwe Isiraeli?+ Kodi ndikusandutsirenji ngati Adima?+ Kodi ndikuchitirenji zofanana ndi zimene ndinachitira Zeboyimu?+ Mtima wanga wasintha+ ndipo pa nthawi imodzimodziyo wadzaza ndi chisoni.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena