Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Muwerenge kuyambira azaka 30+ mpaka 50,+ onse olowa m’gulu la ogwira ntchito+ m’chihema chokumanako.

  • Numeri 8:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 “Lamulo lokhudza Alevi ndi ili: Kuyambira wazaka 25 kupita m’tsogolo azilowa m’gulu la otumikira m’chihema chokumanako.

  • 1 Mbiri 23:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Amenewa ndiwo anali ana a Levi potsata nyumba ya makolo awo.+ Iwowa anali atsogoleri a nyumba ya makolo awo, ndipo mmodzi ndi mmodzi anapatsidwa udindo potsata mndandanda wa mayina awo. Amenewa anali oti azigwira ntchito yotumikira+ panyumba ya Yehova kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena