9 Yesaya anayankha kuti: “Chizindikiro+ chochokera kwa Yehova, chakuti Yehova adzakwaniritsadi mawu amene walankhula, ndi ichi: Kodi mthunzi uyende masitepe 10 kupita kutsogolo, kapena uyende masitepe 10 kubwerera m’mbuyo pamasitepe olowera m’nyumba?”