-
2 Mafumu 7:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Yehova anali atachititsa anthu a mumsasa wa Asiriyawo kumva+ phokoso la magaleta ankhondo, phokoso la mahatchi, ndi phokoso la gulu lalikulu la asilikali amphamvu.+ Choncho anthuwo anauzana kuti: “Taonani! Mfumu ya Isiraeli yaitanitsa mafumu a Ahiti+ ndi mafumu a Iguputo+ kuti abwere kudzamenyana nafe!”
-