1 Mafumu 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Golide+ amene ankabwera kwa Solomo chaka chimodzi, anali wolemera matalente 666,*+ 2 Mbiri 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mfumuyo inachititsa kuti ku Yerusalemu siliva ndi golide akhale wochuluka kwambiri ngati miyala,+ ndiponso kuti matabwa a mkungudza akhale ochuluka kwambiri ngati mitengo yamkuyu+ ya ku Sefela.+ Salimo 68:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chifukwa cha kachisi wanu yemwe ali ku Yerusalemu,+Mafumu adzabweretsa mphatso kwa inu.+ Salimo 72:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye akhale ndi moyo wautali,+ ndipo apatsidwe wina mwa golide wa ku Sheba.+Nthawi zonse anthu azimupempherera.Adalitsike tsiku lililonse.+
15 Mfumuyo inachititsa kuti ku Yerusalemu siliva ndi golide akhale wochuluka kwambiri ngati miyala,+ ndiponso kuti matabwa a mkungudza akhale ochuluka kwambiri ngati mitengo yamkuyu+ ya ku Sefela.+
15 Iye akhale ndi moyo wautali,+ ndipo apatsidwe wina mwa golide wa ku Sheba.+Nthawi zonse anthu azimupempherera.Adalitsike tsiku lililonse.+