Yoswa 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kunalinso Gibeoni,+ Rama, Beeroti, Ezara 2:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ana a Rama+ ndi Geba,+ 621. Yesaya 10:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Wadutsa powolokera mtsinje. Usiku agona ku Geba.+ Rama+ wanjenjemera ndipo Gibeya,+ kwawo kwa Sauli, wathawa.
29 Wadutsa powolokera mtsinje. Usiku agona ku Geba.+ Rama+ wanjenjemera ndipo Gibeya,+ kwawo kwa Sauli, wathawa.