Genesis 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chotero Abulamu anamva kuti m’bale wake wagwidwa+ ndipo akupita naye kudziko lina. Atamva zimenezo iye anasonkhanitsa anyamata ake odziwa kumenya nkhondo.+ Anali akapolo ake okwanira 318, obadwira m’nyumba yake.+ Iwo analondola oukirawo mpaka ku Dani.+ Oweruza 18:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kuwonjezera apo, anatcha mzindawo kuti Dani, kutengera dzina la bambo awo lakuti Dani,+ amene anali wobadwa kwa Isiraeli.+ Ngakhale zili choncho, dzina loyamba la mzindawo linali Laisi.+ Oweruza 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chotero ana onse a Isiraeli anatuluka,+ kuchokera ku Dani+ mpaka kumunsi ku Beere-seba,+ ndipo khamu lonselo linasonkhana pamodzi mogwirizana+ kwa Yehova ku Mizipa,+ pamodzinso ndi anthu a m’dera la Giliyadi.+
14 Chotero Abulamu anamva kuti m’bale wake wagwidwa+ ndipo akupita naye kudziko lina. Atamva zimenezo iye anasonkhanitsa anyamata ake odziwa kumenya nkhondo.+ Anali akapolo ake okwanira 318, obadwira m’nyumba yake.+ Iwo analondola oukirawo mpaka ku Dani.+
29 Kuwonjezera apo, anatcha mzindawo kuti Dani, kutengera dzina la bambo awo lakuti Dani,+ amene anali wobadwa kwa Isiraeli.+ Ngakhale zili choncho, dzina loyamba la mzindawo linali Laisi.+
20 Chotero ana onse a Isiraeli anatuluka,+ kuchokera ku Dani+ mpaka kumunsi ku Beere-seba,+ ndipo khamu lonselo linasonkhana pamodzi mogwirizana+ kwa Yehova ku Mizipa,+ pamodzinso ndi anthu a m’dera la Giliyadi.+