Luka 23:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Atatero anabwerera kukakonza zonunkhiritsa ndi mafuta onunkhira.+ Komabe pa tsiku la sabata+ anapuma malinga ndi chilamulo. Yohane 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho Yesu anati: “M’lekeni, achite mwambo umenewu pokonzekera tsiku limene ndidzaikidwe m’manda.+ Maliko 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho tsiku la sabata+ litapita, Mariya Mmagadala,+ Mariya mayi wa Yakobo, ndi Salome anagula zonunkhira kuti akapake thupi la Yesu.+ Yohane 19:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Choncho iwo anatenga mtembo wa Yesu n’kuukulunga ndi nsalu zamaliro zonunkhira,+ malinga ndi mwambo umene Ayuda anali kutsatira poika maliro.
56 Atatero anabwerera kukakonza zonunkhiritsa ndi mafuta onunkhira.+ Komabe pa tsiku la sabata+ anapuma malinga ndi chilamulo.
7 Choncho Yesu anati: “M’lekeni, achite mwambo umenewu pokonzekera tsiku limene ndidzaikidwe m’manda.+
16 Choncho tsiku la sabata+ litapita, Mariya Mmagadala,+ Mariya mayi wa Yakobo, ndi Salome anagula zonunkhira kuti akapake thupi la Yesu.+
40 Choncho iwo anatenga mtembo wa Yesu n’kuukulunga ndi nsalu zamaliro zonunkhira,+ malinga ndi mwambo umene Ayuda anali kutsatira poika maliro.