Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 29:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 “Zimene uzipereka paguwa lansembelo ndi izi: ana a nkhosa a chaka chimodzi, awiri pa tsiku nthawi zonse.+

  • Levitiko 23:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 “‘Zimenezi ndizo zikondwerero+ za Yehova zimene muyenera kulengeza monga misonkhano yopatulika+ yoperekera nsembe zotentha ndi moto+ kwa Yehova. Imeneyi ndiyo misonkhano yoperekera nsembe zopsereza,+ nsembe zambewu+ ndi nsembe zachakumwa+ motsatira ndandanda ya tsiku ndi tsiku.

  • Numeri 29:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pa tsiku limeneli muzipereka nsembe yopsereza+ yotentha ndi moto yafungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova. Nsembe imeneyo izikhala ya ng’ombe 13 zazing’ono zamphongo, nkhosa zamphongo ziwiri, ndi ana a nkhosa 14 amphongo, ndipo mwana wa nkhosa aliyense azikhala wachaka chimodzi. Muzionetsetsa kuti nyamazi n’zopanda chilema.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena