Levitiko 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “‘Zikondwerero+ za Yehova, kapena kuti misonkhano yopatulika+ imene muyenera kulengeza pa nthawi yake yoikidwiratu+ ndi iyi: Numeri 28:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Ndipo pa tsiku la zipatso zoyambirira,+ pamene muzipereka nsembe yambewu zatsopano kwa Yehova, paphwando lanu la masabata,+ muzichita msonkhano wopatulika. Musamagwire ntchito yolemetsa yamtundu uliwonse pa tsikuli.+ Numeri 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “‘Pa tsiku la 10 la mwezi wa 7 umenewu, muzichita msonkhano wopatulika,+ ndipo muzidzisautsa.*+ Musamagwire ntchito yamtundu uliwonse.+
4 “‘Zikondwerero+ za Yehova, kapena kuti misonkhano yopatulika+ imene muyenera kulengeza pa nthawi yake yoikidwiratu+ ndi iyi:
26 “‘Ndipo pa tsiku la zipatso zoyambirira,+ pamene muzipereka nsembe yambewu zatsopano kwa Yehova, paphwando lanu la masabata,+ muzichita msonkhano wopatulika. Musamagwire ntchito yolemetsa yamtundu uliwonse pa tsikuli.+
7 “‘Pa tsiku la 10 la mwezi wa 7 umenewu, muzichita msonkhano wopatulika,+ ndipo muzidzisautsa.*+ Musamagwire ntchito yamtundu uliwonse.+