Nehemiya 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndinawauzanso mmene dzanja+ la Mulungu wanga lachitira zinthu zabwino kwa ine+ ndiponso mawu amene mfumu inandiuza.+ Pamenepo iwo anati: “Tiyeni timange mpandawo.” Choncho analimbitsa manja awo kuti agwire ntchito yabwinoyi.+ Yesaya 41:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Usachite mantha, pakuti ndili nawe.+ Usayang’ane uku ndi uku mwamantha, pakuti ine ndine Mulungu wako.+ Ndikulimbitsa.+ Ndithu ndikuthandiza.+ Ndikugwira mwamphamvu ndi dzanja langa lamanja+ lachilungamo.’+
18 Ndinawauzanso mmene dzanja+ la Mulungu wanga lachitira zinthu zabwino kwa ine+ ndiponso mawu amene mfumu inandiuza.+ Pamenepo iwo anati: “Tiyeni timange mpandawo.” Choncho analimbitsa manja awo kuti agwire ntchito yabwinoyi.+
10 Usachite mantha, pakuti ndili nawe.+ Usayang’ane uku ndi uku mwamantha, pakuti ine ndine Mulungu wako.+ Ndikulimbitsa.+ Ndithu ndikuthandiza.+ Ndikugwira mwamphamvu ndi dzanja langa lamanja+ lachilungamo.’+