Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 16:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Yamikani Yehova anthu inu, chifukwa iye ndi wabwino,+

      Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+

  • 2 Mbiri 7:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ana onse a Isiraeli anali kuonerera pamene moto unali kutsika, ndiponso pamene ulemerero wa Yehova unaonekera pamwamba pa nyumbayo. Ataona zimenezi, nthawi yomweyo anagwada+ n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi+ ndi kuyamika Yehova, “chifukwa iye ndi wabwino,+ pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhala mpaka kalekale.”+

  • Salimo 73:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 73 Mulungu ndi wabwinodi kwa Isiraeli, kwa anthu oyera mtima.+

  • Salimo 135:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Tamandani Ya, pakuti Yehova ndi wabwino.+

      Muimbireni nyimbo zotamanda dzina lake, pakuti kuchita zimenezi n’kosangalatsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena